2 Akorinto 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse komanso ndidzadzipereka ndi mtima wanga wonse chifukwa cha inu, ndipo ndidzachita zimenezi mosangalala.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda pangʼono? 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:15 Utumiki wa Ufumu,6/2007, tsa. 1 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 219/15/2000, ptsa. 22-23
15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse komanso ndidzadzipereka ndi mtima wanga wonse chifukwa cha inu, ndipo ndidzachita zimenezi mosangalala.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda pangʼono?