Agalatiya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkachita bwino kwambiri mʼchipembedzo cha Chiyuda kuposa anzanga ambiri a fuko langa, omwe anali amsinkhu wanga, chifukwa ndinali wodzipereka kwambiri pa miyambo ya makolo anga.+
14 Ndinkachita bwino kwambiri mʼchipembedzo cha Chiyuda kuposa anzanga ambiri a fuko langa, omwe anali amsinkhu wanga, chifukwa ndinali wodzipereka kwambiri pa miyambo ya makolo anga.+