Agalatiya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 aulule za Mwana wake kudzera mwa ine, nʼcholinga choti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za iye, sindinapite kukakambirana ndi munthu aliyense* nthawi yomweyo.
16 aulule za Mwana wake kudzera mwa ine, nʼcholinga choti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za iye, sindinapite kukakambirana ndi munthu aliyense* nthawi yomweyo.