9 Iwo atazindikira kukoma mtima kwakukulu kumene ndinapatsidwa,+ Yakobo,+ Kefa ndi Yohane, amene anali ngati zipilala, anagwira chanza ineyo ndi Baranaba+ posonyeza kuti agwirizana ndi zoti ife tipite kwa anthu a mitundu ina ndipo iwo apite kwa anthu odulidwa.