Agalatiya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ayuda enawonso anagwirizana naye pochita zachiphamaso* zimenezi. Ngakhale Baranaba nayenso anachita nawo zachiphamasozi.*
13 Ayuda enawonso anagwirizana naye pochita zachiphamaso* zimenezi. Ngakhale Baranaba nayenso anachita nawo zachiphamasozi.*