Agalatiya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ayuda enawonso anagwirizana naye pochita zachiphamaso zimenezi.+ Ngakhale Baranaba+ nayenso anachita nawo zachiphamasozi.
13 Ayuda enawonso anagwirizana naye pochita zachiphamaso zimenezi.+ Ngakhale Baranaba+ nayenso anachita nawo zachiphamasozi.