Aefeso 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamachite zimenezi pokhapokha pamene anthu akukuonani pongofuna kuwasangalatsa,*+ koma ngati akapolo a Khristu amene akuchita chifuniro cha Mulungu ndi mtima wonse.+
6 Musamachite zimenezi pokhapokha pamene anthu akukuonani pongofuna kuwasangalatsa,*+ koma ngati akapolo a Khristu amene akuchita chifuniro cha Mulungu ndi mtima wonse.+