Afilipi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndikalandire mphoto chifukwa ndikudziwa kuti cholinga cha Khristu Yesu pondisankha chinali chimenechi.+
12 Sikuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndikalandire mphoto chifukwa ndikudziwa kuti cholinga cha Khristu Yesu pondisankha chinali chimenechi.+