Afilipi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Si kuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro+ ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndione ngati inenso ndingapeze+ chimene chinachititsanso Khristu Yesu kundipeza.+
12 Si kuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro+ ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndione ngati inenso ndingapeze+ chimene chinachititsanso Khristu Yesu kundipeza.+