Afilipi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikuyesetsa kuti ndikwaniritse cholinga changa chokalandira mphoto.+ Mphoto imeneyi ndi kukakhala ndi moyo kumwamba+ ndipo Mulungu adzaipereka kwa anthu amene anawaitana kudzera mwa Khristu Yesu. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 1111/15/1990, tsa. 25
14 Ndikuyesetsa kuti ndikwaniritse cholinga changa chokalandira mphoto.+ Mphoto imeneyi ndi kukakhala ndi moyo kumwamba+ ndipo Mulungu adzaipereka kwa anthu amene anawaitana kudzera mwa Khristu Yesu.