3 Ndikupempha iwenso wantchito mnzanga weniweni, kuti upitirize kuwathandiza azimayi amenewa. Iwo ayesetsa mwakhama kugwira ntchito yolengeza uthenga wabwino limodzi ndi ine. Achita zimenezi limodzinso ndi Kilementi komanso antchito anzanga ena onse amene mayina awo ali mʼbuku la moyo.+