Afilipi 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo inu Afilipi, mukudziwanso kuti pamene ndinkachoka ku Makedoniya, mutangomva kumene uthenga wabwino, panalibe mpingo ngakhale umodzi umene unathandizana nane pa nkhani ya kupatsa ndi kulandira, kupatulapo inu nokha.+
15 Ndipo inu Afilipi, mukudziwanso kuti pamene ndinkachoka ku Makedoniya, mutangomva kumene uthenga wabwino, panalibe mpingo ngakhale umodzi umene unathandizana nane pa nkhani ya kupatsa ndi kulandira, kupatulapo inu nokha.+