Afilipi 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo inu Afilipi, mukudziwanso kuti pamene ndinayamba kulengeza uthenga wabwino, komanso pamene ndinanyamuka ku Makedoniya, panalibe mpingo ndi umodzi womwe umene unathandizana nane pa nkhani ya kupatsa ndi kulandira, kupatulapo inu nokha.+
15 Ndipo inu Afilipi, mukudziwanso kuti pamene ndinayamba kulengeza uthenga wabwino, komanso pamene ndinanyamuka ku Makedoniya, panalibe mpingo ndi umodzi womwe umene unathandizana nane pa nkhani ya kupatsa ndi kulandira, kupatulapo inu nokha.+