Akolose 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 komanso muzithokoza Atate, amene anapangitsa kuti mukhale oyenerera kulandira nawo cholowa cha oyera+ amene ali mʼkuwala.
12 komanso muzithokoza Atate, amene anapangitsa kuti mukhale oyenerera kulandira nawo cholowa cha oyera+ amene ali mʼkuwala.