Akolose 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Abwera limodzi ndi Onesimo,+ mʼbale wanga wokhulupirika ndi wokondedwa, amene anachokera pakati panu. Iwo adzakuuzani zonse zimene zikuchitika kuno.
9 Abwera limodzi ndi Onesimo,+ mʼbale wanga wokhulupirika ndi wokondedwa, amene anachokera pakati panu. Iwo adzakuuzani zonse zimene zikuchitika kuno.