Akolose 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndamutumiza limodzi ndi Onesimo,+ m’bale wanga wokhulupirika ndi wokondedwa, amene anachokera pakati panu. Amenewa adzakusimbirani zonse zakuno.
9 Ndamutumiza limodzi ndi Onesimo,+ m’bale wanga wokhulupirika ndi wokondedwa, amene anachokera pakati panu. Amenewa adzakusimbirani zonse zakuno.