1 Timoteyo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana ake,+ ankachereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza anthu amene anali pa mavuto+ ndiponso ankagwira modzipereka ntchito iliyonse yabwino. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, ptsa. 6-710/15/1995, tsa. 32
10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana ake,+ ankachereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza anthu amene anali pa mavuto+ ndiponso ankagwira modzipereka ntchito iliyonse yabwino.