2 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika chifukwa cha kuonekera kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu,+ amene wathetsa mphamvu za imfa.+ Komanso pogwiritsa ntchito uthenga wabwino,+ watidziwitsa mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+
10 Koma tsopano izi zatsimikizirika chifukwa cha kuonekera kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu,+ amene wathetsa mphamvu za imfa.+ Komanso pogwiritsa ntchito uthenga wabwino,+ watidziwitsa mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+