-
Aheberi 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Abulahamu anamupatsa chakhumi cha zinthu zonse. Dzina lakeli limamasuliridwa kuti “Mfumu Yachilungamo” komanso mfumu ya Salemu, kutanthauza “Mfumu Yamtendere.”
-