Aheberi 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulahamu anapereka chakhumi cha zinthu zonse kwa iyeyu.+ Tikamasulira dzina lakeli, iye choyamba ndi “Mfumu Yachilungamo,” kenako, mfumu ya Salemu,+ kutanthauza kuti, “Mfumu Yamtendere.”
2 Abulahamu anapereka chakhumi cha zinthu zonse kwa iyeyu.+ Tikamasulira dzina lakeli, iye choyamba ndi “Mfumu Yachilungamo,” kenako, mfumu ya Salemu,+ kutanthauza kuti, “Mfumu Yamtendere.”