Aheberi 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,11/2010, tsa. 21 Nsanja ya Olonda,2/1/1989, tsa. 17
25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+