Aheberi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa ngati magazi a mbuzi ndi a ngʼombe zamphongo+ komanso phulusa la ngʼombe yaikazi,* zimene amawaza nazo anthu odetsedwa, zimawayeretsa mpaka kukhaladi oyera pamaso pa Mulungu,+
13 Chifukwa ngati magazi a mbuzi ndi a ngʼombe zamphongo+ komanso phulusa la ngʼombe yaikazi,* zimene amawaza nazo anthu odetsedwa, zimawayeretsa mpaka kukhaladi oyera pamaso pa Mulungu,+