Aheberi 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose akauza anthu onsewo lamulo lililonse la mʼChilamulo, ankatenga magazi a ngʼombe zazingʼono zamphongo, magazi a mbuzi ndiponso madzi nʼkuwaza bukulo* ndi anthu onse pogwiritsa ntchito ubweya wa nkhosa wofiira kwambiri ndi timitengo ta hisope.
19 Mose akauza anthu onsewo lamulo lililonse la mʼChilamulo, ankatenga magazi a ngʼombe zazingʼono zamphongo, magazi a mbuzi ndiponso madzi nʼkuwaza bukulo* ndi anthu onse pogwiritsa ntchito ubweya wa nkhosa wofiira kwambiri ndi timitengo ta hisope.