Aheberi 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa cha chikhulupiriro, Isaki nayenso anadalitsa Yakobo+ ndi Esau,+ ndipo anawauza zimene zidzachitike mʼtsogolo. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:20 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 13
20 Chifukwa cha chikhulupiriro, Isaki nayenso anadalitsa Yakobo+ ndi Esau,+ ndipo anawauza zimene zidzachitike mʼtsogolo.