Aheberi 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha chikhulupiriro, Yosefe atatsala pangʼono kufa, ananena za kusamuka kwa Aisiraeli, ndipo anapereka malangizo okhudza* mafupa ake.*+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 28
22 Chifukwa cha chikhulupiriro, Yosefe atatsala pangʼono kufa, ananena za kusamuka kwa Aisiraeli, ndipo anapereka malangizo okhudza* mafupa ake.*+