Aheberi 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musasocheretsedwe ndi ziphunzitso zosiyanasiyana zachilendo. Kukoma mtima kwa Mulungu nʼkumene kungakuthandizeni kukhala olimba,* osati zakudya. Chifukwa anthu amene amangoganizira za zakudya,* siziwapindulitsa.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, tsa. 22
9 Musasocheretsedwe ndi ziphunzitso zosiyanasiyana zachilendo. Kukoma mtima kwa Mulungu nʼkumene kungakuthandizeni kukhala olimba,* osati zakudya. Chifukwa anthu amene amangoganizira za zakudya,* siziwapindulitsa.+