-
Aheberi 13:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tsopano abale, ndikukupemphani kuti mumvetsere moleza mtima mawu olimbikitsawa, chifukwa kalata imene ndakulemberaniyi si yaitali.
-