Aheberi 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano, ndikukudandaulirani abale, chonde khalani oleza mtima pamene mukuwerenga mawu olimbikitsawa, chifukwa ndakulemberani kalatayi m’mawu ochepa.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:22 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, tsa. 25
22 Tsopano, ndikukudandaulirani abale, chonde khalani oleza mtima pamene mukuwerenga mawu olimbikitsawa, chifukwa ndakulemberani kalatayi m’mawu ochepa.+