Yakobo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Abale anga, kodi pali phindu lanji ngati wina atanena kuti ali ndi chikhulupiriro koma sachita ntchito zake?+ Kodi chikhulupiriro chimenecho chingamupulumutse?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 14-15 Kukambitsirana, tsa. 97
14 Abale anga, kodi pali phindu lanji ngati wina atanena kuti ali ndi chikhulupiriro koma sachita ntchito zake?+ Kodi chikhulupiriro chimenecho chingamupulumutse?+