-
Yakobo 2:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma wina anganene kuti: “Iweyo uli ndi chikhulupiriro, koma ine ndili ndi ntchito zake. Undionetse chikhulupiriro chako popanda ntchito zake, ndipo ine ndikuonetsa chikhulupiriro changa kudzera muntchito zanga.”
-