Yakobo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma wina anganene kuti: “Iweyo uli ndi chikhulupiriro, koma ine ndili ndi ntchito zake. Undionetse chikhulupiriro chako popanda ntchito zake, ndipo ine ndikuonetsa chikhulupiriro changa mwa ntchito.”+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 15
18 Koma wina anganene kuti: “Iweyo uli ndi chikhulupiriro, koma ine ndili ndi ntchito zake. Undionetse chikhulupiriro chako popanda ntchito zake, ndipo ine ndikuonetsa chikhulupiriro changa mwa ntchito.”+