-
Yakobo 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ganiziraninso za ngalawa. Ngakhale kuti ndi zazikulu kwambiri ndipo zimayenda mokankhidwa ndi mphepo zamphamvu, munthu amene akuziyendetsa amaziwongolera ndi thabwa lalingʼono kwambiri kuti zipite kumene iye akufuna.
-