Yakobo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’chimodzimodzinso ngalawa. Ngakhale kuti ndi zazikulu kwambiri ndipo zimayenda mokankhidwa ndi mphepo zamphamvu, munthu woziyendetsa amaziwongolera ndi thabwa laling’ono+ kuti zipite kumene iye akufuna. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 16
4 N’chimodzimodzinso ngalawa. Ngakhale kuti ndi zazikulu kwambiri ndipo zimayenda mokankhidwa ndi mphepo zamphamvu, munthu woziyendetsa amaziwongolera ndi thabwa laling’ono+ kuti zipite kumene iye akufuna.