1 Petulo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, mukusangalala kwambiri ngakhale kuti panopa nʼkoyenera kuti muvutike kwa kanthawi chifukwa cha mayesero osiyanasiyana+ amene mukukumana nawo. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, ptsa. 12-135/15/1998, tsa. 16
6 Pa chifukwa chimenechi, mukusangalala kwambiri ngakhale kuti panopa nʼkoyenera kuti muvutike kwa kanthawi chifukwa cha mayesero osiyanasiyana+ amene mukukumana nawo.