1 Petulo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza Khristu anavutika pa nthawi imene anali munthu,+ nanunso konzekerani pokhala ndi maganizo ofanana ndi amene Khristu anali nawo. Zili choncho chifukwa munthu amene akuvutika ndiye kuti anasiya kuchita machimo.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,12/1/1986, ptsa. 26-27
4 Popeza Khristu anavutika pa nthawi imene anali munthu,+ nanunso konzekerani pokhala ndi maganizo ofanana ndi amene Khristu anali nawo. Zili choncho chifukwa munthu amene akuvutika ndiye kuti anasiya kuchita machimo.+