1 Petulo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho, pakuti Khristu anavutika m’thupi,+ nanunso dzikonzekeretseni ndi maganizo omwewo,+ chifukwa munthu amene wavutika m’thupi walekana nawo machimo,+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,12/1/1986, ptsa. 26-27
4 Choncho, pakuti Khristu anavutika m’thupi,+ nanunso dzikonzekeretseni ndi maganizo omwewo,+ chifukwa munthu amene wavutika m’thupi walekana nawo machimo,+