Aroma 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Momwemonso inuyo dzioneni ngati akufa+ ku uchimo koma amoyo+ kwa Mulungu mwa Khristu Yesu. 1 Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+
6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+