Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+ 1 Petulo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho, pakuti Khristu anavutika m’thupi,+ nanunso dzikonzekeretseni ndi maganizo omwewo,+ chifukwa munthu amene wavutika m’thupi walekana nawo machimo,+
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+
4 Choncho, pakuti Khristu anavutika m’thupi,+ nanunso dzikonzekeretseni ndi maganizo omwewo,+ chifukwa munthu amene wavutika m’thupi walekana nawo machimo,+