Aroma 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa munthu amene wafa wamasuka ku uchimo wake.+ 2 Akorinto 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti chikondi chimene Khristu ali nacho chimatikakamiza, chifukwa tatsimikiza kuti munthu mmodzi anafera anthu onse,+ chifukwatu onsewo anali atafa kale. Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.
14 Pakuti chikondi chimene Khristu ali nacho chimatikakamiza, chifukwa tatsimikiza kuti munthu mmodzi anafera anthu onse,+ chifukwatu onsewo anali atafa kale.
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.