2 Petulo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene alibe makhalidwe amenewa ndi wakhungu, watseka maso ake kuti asaone kuwala+ ndipo waiwala kuti anayeretsedwa ku machimo+ omwe ankachita kalekale. 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 11
9 Munthu amene alibe makhalidwe amenewa ndi wakhungu, watseka maso ake kuti asaone kuwala+ ndipo waiwala kuti anayeretsedwa ku machimo+ omwe ankachita kalekale.