1 Yohane 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ngati mukudziwa kuti iye ndi wolungama, ndiye kuti mukudziwanso kuti aliyense wochita zinthu zabwino anabadwa kuchokera kwa Mulungu.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:29 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, ptsa. 15-30
29 Ngati mukudziwa kuti iye ndi wolungama, ndiye kuti mukudziwanso kuti aliyense wochita zinthu zabwino anabadwa kuchokera kwa Mulungu.+