Yuda 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Okondedwa, ndinkafunitsitsa kukulemberani za chipulumutso chimene tonsefe tili nacho.+ Komabe, ndaona kuti ndi bwino ndilembe zokulimbikitsani kumenya mwamphamvu nkhondo ya chikhulupiriro+ chomwe chinaperekedwa kamodzi kokha* kwa oyerawo. Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3 Utumiki Komanso Moyo Wathu,11/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, ptsa. 21-226/1/2000, ptsa. 12-136/1/1998, ptsa. 14-199/1/1997, ptsa. 13-142/1/1996, tsa. 79/15/1989, ptsa. 6-7
3 Okondedwa, ndinkafunitsitsa kukulemberani za chipulumutso chimene tonsefe tili nacho.+ Komabe, ndaona kuti ndi bwino ndilembe zokulimbikitsani kumenya mwamphamvu nkhondo ya chikhulupiriro+ chomwe chinaperekedwa kamodzi kokha* kwa oyerawo.
3 Utumiki Komanso Moyo Wathu,11/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, ptsa. 21-226/1/2000, ptsa. 12-136/1/1998, ptsa. 14-199/1/1997, ptsa. 13-142/1/1996, tsa. 79/15/1989, ptsa. 6-7