Chivumbulutso 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mngelo wina akukwera kuchokera kotulukira dzuwa,* ali ndi chidindo cha Mulungu wamoyo. Iye anafuula mokweza mawu kwa angelo 4, amene anapatsidwa mphamvu zowononga dziko lapansi ndi nyanja aja, Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 115
2 Ndinaonanso mngelo wina akukwera kuchokera kotulukira dzuwa,* ali ndi chidindo cha Mulungu wamoyo. Iye anafuula mokweza mawu kwa angelo 4, amene anapatsidwa mphamvu zowononga dziko lapansi ndi nyanja aja,