Chivumbulutso 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mngelo wina akukwera kuchokera kotulukira dzuwa,+ ali ndi chidindo cha Mulungu+ wamoyo. Iye anafuula mokweza mawu, kwa angelo anayiwo, amene anapatsidwa mphamvu zowononga dziko lapansi ndi nyanja. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 115
2 Ndinaonanso mngelo wina akukwera kuchokera kotulukira dzuwa,+ ali ndi chidindo cha Mulungu+ wamoyo. Iye anafuula mokweza mawu, kwa angelo anayiwo, amene anapatsidwa mphamvu zowononga dziko lapansi ndi nyanja.