-
Chivumbulutso 19:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya komanso timupatse ulemerero, chifukwa ukwati wa Mwanawankhosa wafika ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.
-