-
Chivumbulutso 20:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 ndipo adzatuluka kukasocheretsa mitundu ya anthu kumakona onse 4 a dziko lapansi. Mitunduyo ndi Gogi komanso Magogi ndipo adzaisonkhanitsa pamodzi kuti amenye nkhondo. Iwo ndi ochuluka ngati mchenga wakunyanja.
-