Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 71 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 147/15/2007, tsa. 54/1/1999, tsa. 16
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+
35:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 71 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 147/15/2007, tsa. 54/1/1999, tsa. 16