Genesis 46:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini anali Bela,+ Bekeri,+ Asibeli, Gera,+ Namani,+ Ehi, Rosi, Mupimu,+ Hupimu+ ndi Aridi. Genesis 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Benjamini adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ M’mawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zimene wafunkha.”+ Deuteronomo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwa Benjamini anati:+“Wokondedwa+ wa Yehova akhale m’chitetezo cha Mulungu,+Pamene akumutchinjiriza tsiku lonse,+Ndipo iye akhale pakati pa mapewa ake.”+
21 Ana a Benjamini anali Bela,+ Bekeri,+ Asibeli, Gera,+ Namani,+ Ehi, Rosi, Mupimu,+ Hupimu+ ndi Aridi.
27 “Benjamini adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ M’mawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zimene wafunkha.”+
12 Kwa Benjamini anati:+“Wokondedwa+ wa Yehova akhale m’chitetezo cha Mulungu,+Pamene akumutchinjiriza tsiku lonse,+Ndipo iye akhale pakati pa mapewa ake.”+