Genesis 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewa ndiwo anali ana a Esau kapena kuti Edomu,+ ndi mafumu awo.