Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+ Genesis 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+ Malaki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+
3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+
3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+